KHOLA LAPANSI
KHOLA LAPANSI
Khola ili ndi lotchipa chifukwa zipangizo zake zimapezeka mosavuta. Koma pomanga muyenera kuyika mabowo kuzungulira kholalo kuti mpweya ndi kuwala zizirowa m’khola. Kholali limatha kukhala la njerwa kapena mitengo.
Ziwopsezo zake
- Mu khola la pansi mpweya umakhala ochepa chifukwa umakanika kulowa ndikutuluka.
- Matenda amachuluka komaso tizilombo timaswana msanga.
- Afisi ndi mbava amagwira ziweto mosavuta mu khola la pansi.
Mlingo wa Khola La Njerwa