MAVUTO PA KALIMIDWE KOMANSO KAGWIRITSIDWE NTCHITO KA CHAM'MWAMBA
MAVUTO PA KALIMIDWE KOMANSO KAGWIRITSIDWE NTCHITO KA CHAM’MWAMBA
- Ngati tamwa cham’mwamba ngati mankhwala tisanadye, timatha kupanga chizungulire
- Mitengo ya cham’mwamba, makamaka imene ili yaying’ono, imayenera kutetezedwa ku ziweto, makamaka mbuzi
- Alimi ambiri sanaphunzitsidwe za ubwino, kakonzedwe komanso kagwiritsidwe ntchito ka cham’mwamba
- M’madera ena, kupeza misika ndi kovuta.