MALO OMWE MALAMBE ANGADZALIDWE
MALO OMWE MALAMBE ANGADZALIDWE
- Malo otentha ngati a mphepete ya nyanja ya Malawi
- Angadzalidwe m`minda, m`mbali mwa munda kapenanso m`madimba ngati mukufuna kumakolola masamba
- Angathenso kudzalidwa pa malo woti mbeu zina sizichita bwino.