KUKOLORA
KUKOLORA
Zinthu zosiyanasiyana zintha kupezeka kuchokera kumtengo wamalambe monga masamba, zipatso ndikhungwa (luzi)
Masamba: amapanga ndiwo kapena mankhwala
Khungwa: amachotsako luzi komanso mankhwala
Zipatso: Chipatso chokhwima chimakhala ndi chigoba chopitira ku chikasu ndipo mkati mumakhala ufa oyera ndi mbewu zokhwima. Ku Malawi kuno malambe amakhwima kuyambira mwezi wa May.
Malambe wokhwima bwino
- Pokolola zipatsozi mutha kutola ndi manja, kugwiritsa ntchito mtengo wautali pokola zipatso