UBWINO WA NANDOLO
UBWINO WA NANDOLO
- Ndichakudya cha m’mgulu la nyemba
- Amabweretsa ndalama
- Alimi atha kudyetsera nandolo ziweto
- Nandolo amabwenzeretsa chonde mu nthaka
- Mizu ya nandolo imakaphwanya nthaka yolimba yomwe imapezeka pansi pa dothi lapamwamba.