ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

KUKOLORA

KUKOLORA

Zinthu zosiyanasiyana zintha kupezeka kuchokera kumtengo wamalambe monga masamba, zipatso ndikhungwa (luzi)

Masamba: amapanga ndiwo kapena mankhwala

Khungwa: amachotsako luzi komanso mankhwala

Zipatso: Chipatso chokhwima chimakhala ndi chigoba chopitira ku chikasu ndipo mkati mumakhala ufa oyera ndi mbewu zokhwima. Ku Malawi kuno malambe amakhwima kuyambira mwezi wa May.

Malambe wokhwima bwino

  • Pokolola zipatsozi mutha kutola ndi manja, kugwiritsa ntchito mtengo wautali pokola zipatso
Share this Doc