ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

MAVUTO PA KALIMIDWE KOMANSO KAGWIRITSIDWE NTCHITO KA CHAM'MWAMBA

MAVUTO PA KALIMIDWE KOMANSO KAGWIRITSIDWE NTCHITO KA CHAM’MWAMBA

  • Ngati tamwa cham’mwamba ngati mankhwala tisanadye, timatha kupanga chizungulire
  • Mitengo ya cham’mwamba, makamaka imene ili yaying’ono, imayenera kutetezedwa ku ziweto, makamaka mbuzi
  • Alimi ambiri sanaphunzitsidwe za ubwino, kakonzedwe komanso kagwiritsidwe ntchito ka cham’mwamba
  • M’madera ena, kupeza misika ndi kovuta. 
Share this Doc