KUGULITSA MBUZI KWA PHINDU
KUGULITSA MBUZI KWA PHINDU
Ubwino wogulitsa ziweto kudzera mmagulu
- Mbuzi nthawi zambiri zimagulitsidwa m’misika yopanda dongosolo lenileni kotero alimi sapeza phindu lokwanira.
- Kotero ndikwabwino kupanga maguru ogulitsira ziweto zanu ku makampani kapena ku tauni pamitengo yabwino komanso pochepetsa zolowa kufikira misikayi
- Pezani njira zina zopezera ndalama kusiyana ndi kugulitsa ziweto zanu motsika mtengo pamene mwakumana ndi vuto.
- Komanso khalani ndi njira zina zopezera ndalama monga; ulimi wambewu, mabanki mkhonde ndi njira zina.