ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

MBUZI ZA CHIZUNGU

MBUZI ZA CHIZUNGU

Ubwino

  1. Zimakula mwa changu
  2. Zimakhala ndi nyama yambiri
  3. Zimagulitsidwa pa mtengo wokwera kuyerekeza ndi za makolo.

Ziwopsezo pa malonda a Mbuzi za Chizungu

  1. Ndalama zolowa zimakhala zochuluka pa zakudya, malo ogona komanso posamalira ku matenda poyerekeza ndi Mbuzi za makolo
  2. Sizimapilira ku matenda opezeka kuno ku Malawi
  3. Zimafunikira ukadawulo wapadera wowetera kuti mlimi apeze phindu lochuluka.
Share this Doc