ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

TIZIROMBO

TIZIROMBO

ZIZINDIKIRO

KUPEWA NDI KUTETEZA

Nyongolotsi

  • Kutupa mimba ndi sagwada
  • Kutsekula m’mimba
  • Khungu lokwinyata
  • Kuchepa magazi.
  • Mwetsani kapena bayani mankhwala a nyongolotsi kumayambiriro ndi kumapeto a nyengo ya dzinja
  • Msabata zitatu olo zinayi zili zonse mu dzinja sinthani dambo lodyetsera ziweto
  • Chotsani ndowe m’khola tsiku lililonse
  • Onetsetsani kuti ng’ombe za chichepere zili ndi chakudya chokwanira
  • Zomwera madzi zikhale za ukhondo.

Hardware Disease

  • Imakhala yonyentchera ngati ili ndi matenda a chifuwa chachikulu (TB).
  • Siidya mokwanira chifukwa mapepala a pulasitiki amadzadza m’mimba ndiye imamva ngati yakhuta kale
  • Imavutika ikamayenda chifukwa imamva ululu.
  • Onetsetsani kuti chakudya ng’ombe zanu chiribe mapepala a pulasitiki, masaka kapena zitsulo.
Share this Doc