KAGULITSIDWE KA UCHI
KAGULITSIDWE KA UCHI
Uchi umagulitsidwa mosiyanasiyana kutengera mtundu wa makasitomala ndi malo omwe ukupezekera.
- Kugulitsa m’njira yowodetsana: – mlimi kugulitsa kwa ogulitsa, ndipo njirayi ogula amatenga uchi wochuluka kwa alimi.
- Kugulitsa mwapang`ono-pang`ono: – mlimi amapakira mabotolo ndi kumagulitsa pakhomo kapena m’misika ing’onoing’ono ya m’mudzi kwa ogwiritsa ntchito.