ZOFUNIKA PA ULIMI WA NJUCHI
ZOFUNIKA PA ULIMI WA NJUCHI
Zipangizo zofunika paulimi wa njuchi.
- Ming’oma
- Zovala zozitetezera
- Chiuzilira utsi
- Cheyo
- Ndowa
- Chofinyira uchi
- Mpeni
- kope
- Khasu
- Zikwanje
- Majombo/ gumboots
- Magalavu.
Docy
ZOFUNIKA PA ULIMI WA NJUCHI
Zipangizo zofunika paulimi wa njuchi.