ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

ZOVUTA PA ULIMI WA NJUCHI

ZOVUTA PA ULIMI WA NJUCHI

  • Njuchi zimaluma: Anthu ena zikawaluma amatuluka zotupa pa thupi ena kufa kumene
  • Kubedwa ndi kuonongedwa kwa ming’oma
  • Kusalowa ndi kusamukasamuka kwa njuchi m’ming`oma.
Share this Doc