ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

KUSANKHA MALO OLIMAPO NANDOLO

KUSANKHA MALO OLIMAPO NANDOLO

  • Sankhani malo a dothi la chonde komanso lotaya madzi
  • Nandolo samachita bwino pa malo a lowe
  • Pewani kubzala nandolo malo a chipalawe (a dothi la mchere) chifukwa nandolo sachita bwino.

KUKONZA M’MUNDA

  • Tipulani/gaulani m’munda mwanu bwino kuti musunge nthaka ndi chinyontho
  • Thirani manyowa m’munda pa milungu iwiri kapena inayi nthawi yobzala isanafike
  • Pangani mizere yotalikirana 75cm kapena 90cm.
Share this Doc