KUKONZEKERA ULIMI WA MTEDZA
KUKONZEKERA ULIMI WA MTEDZA
Kukonza munda
-
Sankhani nthaka yachonde, yotaya madzi ndipo malo ake asakhale wotsetsereka kwambiri
-
Pewani malo a mphanje
-
Konzani munda mvula yobzalira isanagwe kuti mubzale moyambirira.