ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

MIZERE

MIZERE

  • Gaulani mozamitsa masentimita 25 mpaka 30

  • Undani mizere yachithasathasa pamwamba kuti mzere ukhale ndi mikwasa iwiri

  • Chithasathasa chikhale chokula masentimita 30

  • Undani mizere motalikirana masentimita 75 kuchokera pakati pa mzere ndi unzake

  • Mzere ukhale wotalika masentimita 30 kuchokera pansi kufika pamwamba

Mikwasa italikirane masentimita 20 komanso ikhale masentimita 5 kuchokera ku mphepete kwa mzere.

Share this Doc