ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

KUSENDA NDI KUSANKHA

KUSENDA NDI KUSANKHA

  • Sendani mtedza pokhapokha ngati mukufuna kuugwiritsa ntchito

  • Sendani mtedza wouma bwino ndi manja kapena makina

Makina oswera/ osendera mtedza

  • Musawaze madzi posenda mtedza chifukwa madzi amayambitsa chuku

  • Mtedza wa nkhungu ndi chuku umavuta malonda komanso umayambitsa matenda a khansa yam’chiwindi

  • Musadyetse ziweto mtedza wa chuku

  • Mphwemphwa zikhale pazokha.

Share this Doc