CHIMANGA
CHIMANGA
Zoyenera Kudziwa Paulimi Wachimanga
Chimanga chimakula bwino mu nthaka yosasunga madzi, nthaka ya chonde, komanso kumadela komwe mvula imagwa kudutsa ma milimita 500.
Pewani:
- Malo owuma
- Malo osunga madzi
- Nthaka yosagwirana bwino
- Madera wotentha kwambiri kupitilira 38 °C.