ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

KUBZALA

KUBZALA 

Kukonzekera

Pezani mbeu yamakono, yovomerezeka komanso yogwirizana ndi dera lanu. Funsani alangizi a zaulimi za mtundu wa mbeu womwe umachitabwino m’dera lanu.

Bzalani 20 kilogalamu pa hekitala mbeu ya chimanga yaing’onoing’ono. Kapena 25 kilogalamu pa hekitala mbeu ya chimanga yaikuluikulu. .

Dzalani motere, pamizere yotalikirana ma sentimita 75, mapando otalikirana ma sentimita 25 dzalani chimanga chimodzi

Pakizani pasanapite masiku asanu ndi awiri (7) mbeu zitamera.

Share this Doc