KUKOLOLA
KUKOLOLA
Kororani chimanga munthawi yoyenera pamene chauma kuti chisaonongeke. Chimanga chikafikapo poti chikololedwe chimaweramira pansi.
Kuunjika pa mulu oima (mitoro) ndikofunika pothandizira kuti chimanga chiume mwansanga ndipo zimathandizira alimi kuyamba kugalauza pomwe nthaka idakali yachinyontho.
Kororani chimanga msanga mukaika pa mitoro poteteza mbewa, chiswe komanso anakafumbwe m’munda ndipo chitengereni kunyumba mosamala.