KUTONORA NDI KUSANKHA
KUTONORA NDI KUSANKHA
Mutha kugwiritsa ntchito zipangizo zamakono zotonorera kapena pamanja, koma onetsetsani kuti mbewuzi ndizouma bwino.
Petani chimanga chanu kuti muchotse zinyalala. Sankhani chimanga chanu ndi kuchotsa choola ndi choonongeka. Chimanga chosankha bwino chimakhala ndi mtengo wokwererapo pa msika.
Makina opetera chimanga
Thirani mankhwala oyenerera kuti muteteze mbeu zanu ku namkafubwe kapena sungani chimanga mumatumba aja a hermatic osafuna mankhwala.
Thumba la hermatic losafuna mankhwala