KUPALIRA
KUPALIRA
-
Ndibwino kuti m’munda wa mtedza usakhale ndi tchire
-
Palirani kosachepera kawiri; palirani pakapita masiku 20 chibzalireni kenako masiku 50 chibzalireni.
-
Zulani udzu ndi manja pamene mtedza wayamba maluwa ndi kuika
-
Mukhoza kuthira mamkhwala opha njere za udzu kapena udzu umene.
-
Valani modziteteza pothira mankhwala
-
Njira ngati kasinthasintha wa mbewu pamunda, kudyetsa ziweto m’munda nthawi ya chilimwe komanso kugalawuza mozama kumachepetsa udzu m’munda.