KUSENDA NDI KUSANKHA
KUSENDA NDI KUSANKHA
-
Sendani mtedza pokhapokha ngati mukufuna kuugwiritsa ntchito
-
Sendani mtedza wouma bwino ndi manja kapena makina
Makina oswera/ osendera mtedza
-
Musawaze madzi posenda mtedza chifukwa madzi amayambitsa chuku
-
Mtedza wa nkhungu ndi chuku umavuta malonda komanso umayambitsa matenda a khansa yam’chiwindi
-
Musadyetse ziweto mtedza wa chuku
-
Mphwemphwa zikhale pazokha.