MIZERE
MIZERE
-
Gaulani mozamitsa masentimita 25 mpaka 30
-
Undani mizere yachithasathasa pamwamba kuti mzere ukhale ndi mikwasa iwiri
-
Chithasathasa chikhale chokula masentimita 30
-
Undani mizere motalikirana masentimita 75 kuchokera pakati pa mzere ndi unzake
-
Mzere ukhale wotalika masentimita 30 kuchokera pansi kufika pamwamba
Mikwasa italikirane masentimita 20 komanso ikhale masentimita 5 kuchokera ku mphepete kwa mzere.