MTEDZA
MTEDZA
Ubwino wa mtedza
-
Mtedza ndi chakudya chimene muli michere yofunikira ku thupi la munthu monga mavitamini, mafuta komanso zomanga thupi
-
Mtedza umabwezeretsa chonde m’nthaka
-
Mtedza umabweretsa ndalama tikagulitsa
-
Masangwe ake ndi chakudya chabwino cha ziweto komanso kupangira manyowa.