ZAULIMI APP

ZAULIMI APP

Making Agricultural Extension Services Easily Available

Docy

KUGULITSA NANDOLO

Kugulitsa Nandolo.

  • Gulitsani nandolo wosankha bwino
  • Gulitsani nandolo wanu ku misika yoyenera pa mtengo wosachepera mitengo yokhazikitsa boma
  • Ngati alimi alipo ochuluka, memani anzanu kuti mugulitse pa gulu pa mtengo wabwino
  • Ngati muli mu bungwe la alimi pezani nokha msika wodalirika.
  • Afunseni alangizi a ACE kuti akuthandizeni kusaka misika
Share this Doc