KUSANKHA NDI KUSUNGA
KUSANKHA NDI KUSUNGA
- Sankhani nandolo wanu bwino pochotsa nandolo ofota,osweka ndi wamtundu wina
- Umitsani nandolo wanu moyenerera
- Sungani nandolo wanu pamalo pouma komanso podutsa mphepo
- Ndikofunika kuthira makhwala oteteza ku tizirombo towononga nandolo pamalo osungirapo
Weyahausi yosungirako nandolo