KUSANKHA NDI KUKONZA MALO
KUSANKHA NDI KUKONZA MALO
Kusankha malo
Sankhani nthaka ya chonde yotaya madzi.
- Pewani malo omwe panalimidwako soya kapena fodya zaka ziwiri zapitazo
- Pewani kubzala soya pamalo otsetsereka, wosunga madzi, a mchenga wambiri komanso pa mnthuzi.
Kusosa
Sosani pogwiritsa ntchito zikwanje, zigwandali ndi makasu.