KUSANKHA SOYA
KUSANKHA SOYA
Cholinga chosankhira mbewu ndikukhala ndi mbewu kapena zokolola zomwe zili zopanda matenda, zosasweka, zosadyedwa ndi tizilombo, zosapyapyala, zopanda zitsotso ndi zina zosafunikira.
Dziwani kuti mbewu yamaonekedwe abwino imakhalaso ndi msika wabwino. Mungathe kupeta kapena kugwiritsa ntchito zida zina ngati zomwe zikuwoneka pazithunzipa.
Makina Opetera Soya