MIZERE
MIZERE
Mungathe kubzala soya pa mizere kapena pa mabedi a thyathyathya
Konzani mizere yotalikirana masentimita 75 kuti mudzabzale pa mikwasa iwiri yotalikirana masentimita 20.
- Mungathe kukonza mabedi a thyathyanthya kuti mudzabzale pa mikwasa yotalikirana masentimita 45.